LYRIC
[ad_1]
Osanama iwe wekha umakwana
Kukutobwanya ngati kutobwanya mwana
Thupi kufewa
kodi mafuta omwewa
Ndiri pa easy ena aphula njerwa
Ukamachoka mthupi mwanga mumachema
Ndimakonda kukuyang’ana ngati kanema
Ndipatse nkono uvine ndi angozo
Mahope akowo uwauze no go zone
Kunditchula sweet ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mammawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Babe umakwana
Kunditchula sweet ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mammawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Dale umakwana
Tikumva kukoma andimva madzi chaka chino
Akumva kuwawa angokhalira cafenol
Mutu kuphwanya akungotuluka kamfuno
Sakumagona akumwa mankhwala a tulo
Wandiloka
koma apa palibe kuchoka
Wandifowola
Mphamvu zanga apa zikushota
Wandiloka
koma apa palibe kuchoka
Wandifowola
Mphamvu zanga apa zikushota
Kunditchula sweet ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mamawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Babe umakwana
Kunditchula sweet ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mamawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Dale umakwana
Kunditchula sweet ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mammawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Babe umakwana
Kunditchula sweet ngakhale titayambana
Kuoneka pretty olo ukudzuka mammawa
Umakwana
Iwe umakwana
Umakwana
Dale umakwana
[ad_2]
No comments yet